Udikilebe Lyrics
- Genre:Indie
- Year of Release:2024
Lyrics
Udikilebe - Amidu Ellan
...
uziyendaaa
eeeh uziyenda
eya uziyenda
pakulila uziyenda
it's 3 in the morning ndazuka ndichitulo
ndiwerenge then nkalowe nklasi 7:30
eya ndasambila surf kuno
breakfast abale kulibe kunoo
kuimbila 4n kunyumba kungopeleka Moni
akuti zinthu sizili bwino
ati hello mwanawe tuuziwa suli bho
koma kunoso zinthu nde sizikuyenda
tingokhalila madeya fungo la mgaiwa tumvela kwa neba
ndeno udikilebe komanso tipemphelebe
wakumwamba amadyesa njiwa ndi mileme
kukisiya sizingatheke
ndati udikilebe iwe
komanso tipemphelebe
wakumwamba amadyesa njiwa ndi mileme
nde kukusiya sizingatheke
lira kom uziyenda iwe
ulile kom uziyenda
poti tili pa mtunda pa mtunda komabe kaziyenda
kusogoloko kuli msetse mwanawe
ndiyeno kaziyenda
lira kom uziyenda iwe
ulile kom uziyenda
poti tili pamtunda mwananga komabe kaziyenda
kusogoloko kuli msetse mwanawe komabe ndiyeno kaziyenda aaah
ukukumana ndi zokhoma
moyo wako sukumva kukoma
uli ndi degree sizuyenda
anzako akusangalala everyday kom alibe olo diploma
eya that's how life goes uliphuzile ziko just carry on osadodoma
nde ukaputhwa lilapo eya siwe robot kom osaima my dear
muli ma ups and down
munjilamu muli miyala ,muli minga, muli njoka
muli ma ups and down ooh my God
muli miyala ,minga ndinso njokaa
by wilton