Amama ft. Goddy Zambia Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Yeah I'm Mr Blaq Eti
Chelaaa
Nsaka yamike mukalowa mumanda Amai
Zomwe mwandi chitila nithikodza Inu Amai
Sindidziwa mothokozela
Mafuno anga munandi konzela munandi konzela
Amama nkuti zikomo amama
Nimadziwa mumandi konda mumandi konda amama
Ndidziwa sikambili nimaku udzani koma ponse neh I mean it
Ndipo chikondi chanu nthawi zonse neh I feel it
Amma munandi sunga neh kuti nikule
Mwana wanu Ali bwino kuno Musa dandaule
I am working hard for you ndine olimba amama
I learnt this from you ndimwe olimba amama
Mumani pemphelela ambuye ankale nane
Muli kuti sunga ine akulu na adumbu bane
Ndizambili inu munandi chitila
Ndizambili mukalunichitila
Nde chomwe ndikufuna kuudzani
Pa zonse ine Mai wanga Niku yamikani
Nsaka yamike mukalowa mumanda Amai
Zomwe mwandi chitila nithikodza Inu Amai
Sindidziwa mothokozela
Mafuno anga munandi konzela munandi konzela
Amama nkuti zikomo amama
Nimadziwa mumandi konda mumandi konda amama
Lelo tifuna mudziwe kuti I love you
Kaya komwe tikadakhala without you
Kopanda Inu kunaka khala kanthu
Inu Mai ndinu pillar ya banja lathu
Ndikumbuka paja nkali mwana mukazanda
Nkali mwana nika lakwa muka zanda
Ninalu ganiza kuti mwina ni kundizonda
Koma apa naphunzila ni kunikonda
Ndipemphera ambuye akusungeni amama
I pray that you see me win amama
I pray that the whole family I pray you see the fruits of your labor amama we love you amama
Nsaka yamike mukalowa mumanda Amai
Zomwe mwandi chitila nithikodza Inu Amai
Sindidziwa mothokozela
Mafuno anga munandi konzela munandi konzela