
Pantalonè Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
This song is not currently available in your region.
Try the alternative versions below.
Alternative versions:
Lyrics
Pantalonè - Crispy Malawi
...
Uh-huh Uh-huh
Uh-huh uh-huh uh-huh
Okay
Praise the Lord
Nduwoneka bho ndavala pant alone (Uh-huh)
Met my ex akuti "Mmh you've changed a lot"
The grind don't stop 'till you see the Benz on the parking lot

I had no where to go, big bro didn't like my smokin' habits (habits)
Pano blessings ndi nyanja ngati ndimagona mkachasi (mkachasi)
Hit me up pa den uli ndi ufulu wofukisa tchalisi (tchalisi)
Koma fwaka ndi panja fukwa mkati muno nalesa
Utha kulinka ndi Eli Njuchi ngati ufuna malesa (malesa)
Anthu ena amatha kusintha city utawatenga ku Dedza (ku Dedza)
Koma usazafooke uzizapusha uzabooleza (uzabooleza)
Ngati siwe Jah Jah uli panja sindupembedza (sindupembedza)
Pamalo timatenthetsa (timatenthetsa), matako amagwedeza
So many fishes in the sеa, Koma uziwa dollar ndi m'bedza
I wanna get back to my