
Nyimbo ft. Jeff Nyimbo Lyrics
- Genre:World Music/Folklore
- Year of Release:2024
Lyrics
Ona baby ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Wandipengetsa ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Kungola kukongolako sipanja pokha
Kukongola ndi mtima omwe
Tasendela tasendela pafupi nane
Ndifuna uone
Umandipengetsa
Ukatekesa
Umabebetsa
Umanditethetsa
Umandipengetsa
Ukatekesa
Umatethetsa
Ona baby ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Wandipengetsa ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Zoti Uli kutali sizindikhudza
Akazi ena sandisutha ah sindiwafuna
Ukamasekelela inenso ndimaonetsa mano
Ichi ndi chimvano maso ayamba mwano
Lero ndabwela ndi gitala
Sitisiyana Mpaka umvele nyimbo yanga
Ndipo ukamadzuka uthyole dance
Uthyole dance uthyole dance
Wagwedeza mtima wanga
Momwe umagwedezela
Ona baby ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Wandipengetsa ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Fire on fire on fire on fire on fire
Oh fire
Girl you got me burning
And I'm burning by your fire
Turn up your radio
When you hear this song
Ndayimbila iwe
Turn up the radio
When you hear this song
Ndayimbila iwe
Ona baby ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Wandipengetsa ndakuyimbila nyimbo
Nyimbo
Ndakuyimbila nyimbo
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala
Sinafune kulemba kalata
Olo kuyimba phone
Ndabwela ndi ma gitala