![Hallelujah ft. Lawi](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/10/11/7511d34cdc4340e0b6e85803b49e6991H3000W3000_464_464.jpg)
Hallelujah ft. Lawi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Hallelujah ft. Lawi - Cozizwa
...
Dzuwa likawala
ndikadzuka mamawa ndimangoti
mwandipatsa chimwemwe
kundichotsela nkhawa
ndimangoti
ngakhale dollar yandivuta, sindidanda zamawa ndimangoti
kaya matenda andigwira, thupi lonse kuwawa ndizingoti
Chimwemwe changa siwamba
ndichochokera kumwamba
sichichokera kwina
chifika pansi pamtima
He's given me a new song
ohhhh ohhhh
musandidabwe mukamva(eh)
ohhhh ohhhh
ingondijoyinani!
ohhhh ohhhh
sindzasiya kuyimba
ohhhh ohhhh
He's been too good
He's been too good to me
Hallelujah
Zifukwa ndizambiri zoyimbila
kuchokera pansi pa mtima
Mawu ambili ine ndilibe
Oposera omwewa a hallelujah wa
M'nyengo ya mdima mulinane
Nthawi yachisoni mumakhala nane
Chimwemwe changa sichidza mamawa okha
poti mulinane
tinayala mphasa, mtima mwanga oh
ndipo chisefuka
Hallelujah
oh oh ohh!
ohhhh ohhhh
musandidabwe mukamva
ohhhh ohhhh
ingondijoyinani
ohh ohhh
sindzasiya kuyimba
ohhhhh ohhh
He's been too good to me
poti zingavute bwanji
mudzakhalane nane
awa ndi mawu anu
malonjezano anu
kuchoka pakamwa panu Yahweh
Chimwemwe changa siwamba
ndichochokera kumwamba
sichichokera kwina
chifika pansi pamtima
He's given me a new song
ohhhh ohhhh
musandidabwe mukamva
ohhhhh ohhh
ingondijoyinani
ohhhhh ohhh
sindzasiya kuyimba
He's been too good
He's been too good to me
Sing Hallelujah, sing hallelujah
musandidabwe mukamva
sing Hallelujah, sing hallelujah ingondijoyinani
sing Hallelujah sing hallelujah
sindzasiya kuyimba
sing Hallelujah sing hallelujah
He's been too good
he's been too good to me