Tizipeleke ft. Francis Bwalya Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Tizipeleke kwa Ambuye watu Nyamalenga watu mwine zonse, atuitana akuti bwerani, bwerani ana musacedwe
Pomwe tuna badwa tunachokera kwa Ambuye, anaika ncito zonse muli ife kusonyeza mpavu zake mwine wache, kusonyeza mpavu zake mwine wache
Ntawi zonse pamene tiyenda paziko atouza kunkara bwino ndi anti, ndikubacitila zabwino ntawi zonse, kusonyeza ncito zake muli ife, kankalifwe Katie mdi ncito zatu sisikondweresa timakaika namankalodwe yatu. Ndepo cimalengesa na kucoka pamanso pamulungu, ndipo chimalengesa na kucoka pamanso pamulungu
Nicifukwa cake tibwelere kuli Yesu, Nyamalenga wesu tionese mpavu zace, kuti tilamulile name tionese mpavu ndi Yesu muncito zatu ndimu kumpempera
Pamene mayeso yatufikila Yesu atiuza tizatope kankale mavuto yatufikila Yesu tiuza tizatope