Kondanani Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2019
Lyrics
Kondanani - Rudo Acappella
...
156. Mau Akukwiya Leka
ANGRY WORDS! OH, LET THEM NEVER
1. Mau akukwiya leka, Musanene konsetu;
Muwauze mau onse Asanadetse m’lomowo.
Chorus
Kondananitu, Ati Ambuye, Ana mverani malamulowo;
Kondananitu, Ati Ambuye, Ana mverani lamulo.
2. Cikonditu ndi coyera, Ndi cibwenzi comwenso,
Musaciononge konse Ndi mau akukwiyawo.
3. Maubwenzi amasweka, Ndi mabanja omwenso;
Ka’mba mau a kukwiy aOlankhulidwa