M'bale Wanga Konzekera Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
M'bale Wanga Konzekera - The Golden Vocals Ministry
...
Pomwe yesu aza bwera
kuza tenga antu ache kodi
uzapeka. kodi uzapezeka uli
olungama (ntawi) ija yesu azaza nso.
(mbale)wanga konzekera kubwera
kwa yesu mfumu. (siya) kuchita zoyipa
bwera kwayesu mfumu.
(kubwera kwayesu kulipa fupi tisinte)
on ohoh ohoho oho
(tiyembekezere yesu) azavbwela