Thantwe Latu Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Thantwe Latu - Asante Acappella
...
Mbuye ali thanthwe lathu, Ndiye pothawira pathu;
Atipulumutsa m’zonse, Ndiye pothawira pathu.

Ndiyetu thanthwe lilomba, Ndi mthuzi nthawi yotentha;
Mtsogozi wa aulendo, Ndiye pothawira pathu.

Inu thanthwe lokondedwa, Ndinu pothawira pathu;
Khalani mthangati wathu, Ndinu pothawira pathu.