![Imvani Ine](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/06/24/8a4de770aa0a461c9adea189225b7121_464_464.jpg)
Imvani Ine Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Imvani Ine - Asante Acappella
...
Imvani ine
nalila mbuye mvani
Navutika pa dziko pano mvani ine x2
Imvani ine nalila mbuye mvanix2
Momwe anthu akumwalilamo
Ndipo mutima wanga ukuchita manta
Sindikuziwa komwe ndipitha
Chonde ndena nikela kwa ine
Ndasokonezeka malangililo anga
Ndingomenukila kwa inu mbuya wanga
Chifukwa ndinu oka amene
Muli ndimayanko amene ndikufuna...
(Imvani ine......)
Imvani ne
Nalila mbuye mvani
Navutika pa dziko pano mvani ne x2