Feel Empty (Ndakusowa) Lyrics
- Genre:Dancehall
- Year of Release:2023
Lyrics
Uuuuuh
N'duna you uuuuuh
Trumine aaaaaa ah
Udali ngati mtonthonzi ndikamalira
Sumalora ndigwe pansi umandigwira
Ngakhale pamavuto umapilira
Zoti wanga ndiwe ndimadalira
Koma udangochoka ngati mphepo
Kundisiya ndekha iwe kulibeko
Ndikadwala udali yanga herb
Opanga iwe ndingakhale bwanji ine
Koma pano ndakusowa sowa sowa iwe
Ndimafuna n'mtakuona ona ona ine
Paja umkati amoyo salekana (aaa aah)
Bwanji sitimaonana
Mesa umkati amoyo salekana (aaah aah)
Bwanji sitimakumana (naaa)
Udangondisiya pa dzuwa
Ndimkafunitsitsa tinzalumbire pa guwa (gyal)
Koma udapanga mistake thing
Kundisiya opanda risk et?
Chikondi chakocho ubweretsetso
Zokoma zakozo ubweretsetso girl
Ndatopa kukhala ndekha ineyo
Panopa anthu amandiseka
Mtimawu kukhumba nditakulondora
Ma missing omwewa mpaka kunjenjemera
Kuchoka udachika moti suzabweradi?
Ndikasuma mpaka akwanu akayankha mulandu
Mtimawu
Kuvuta kufuna you
You're present girl it make cool
Yeh, girl you make me cool
Girl you make me cool uh
Pano ndakusowa sowa sowa iwe
Ndimafuna n'mtakuona ona ona ine
Paja umkati amoyo salekana (aaa aah)
Bwanji sitimaonana
Mesa umkati amoyo salekana (aaah aah)
Bwanji sitimakumana
Mtimawu
Kuvuta kufuna you
You're present girl it make cool
Yeh, girl you make me cool
Girl you make me cool
Mtimawu uuuuuh
Kufuna you uuuuuh
Ubwere kuno uuuuh
Udzamalize zinthu uuuuh