![Duwa ft. Hemon](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/05/02/4e27767943a5450eb5824274a0d56cd2_464_464.jpg)
Duwa ft. Hemon Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndinagwada pansi
Kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Love,
Was complicated
Cause I kept chasing the wrong people
That's why my life changed
When you came into the picture
Beauty from ashes
You made out of my heart wreckage
You brought summer into the winter
And flipped the loss script
So, I had to make you my queen
Mwai subwera kawiri
Mphwemphwa ndi zambirimbiri
Zongokonda pamtendere
Ndiku darker ikapenga
Singaphweketse chomwe
Wandipatsa namalenga
Ndipeza wina watenga
Nkusala ndekha pamvula
Mu den yopanda denga
Nde sendera ndikumajor
Si zamovie komabe
Ndikhala wako director
Coordinating this
Divine written future together
You remain steadfast
In the pain and hurdles
Easy to love
Zi ma dinner date pa lake
Komanso ku Nandos
Konse ku park
Okongola kunja ndi ngati
Wandipanikiza ndi chikondi
Cha khathi khathi
The starry skies, remain the witness
Serenading Yah's approval
Of this communion
And divorce is not an option
We ride till the wheels fall
Remains the notion
Through the sticks and stones
Through the peaks and lows
You my ride or die till Yeshua calls
Yeshua is King
Ndinagwada pansi
Kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa
Langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaaa
Chokhumba
Cha Moyo wanga
Ndikuyamika ndalipeza
Langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaa
Chokhumba
Cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa
Talk is cheap
Even when we use expensive mics
But am committed to our love
And doing right
Ikapenga prayer the source
For drawing all our might
Patsogolo ndi Yeshua
Za iweyo ndili shuwa
Nzeru zokhwima ngati tchuwa
Love si chimatchini
Ngati swagga ya achina Vuwa
Sizopanana kukangana, kukakamizana
With you am home free
Ndipo itsanana
Ndiwe kadzuwa
Kuli m'dima unadzetsa masana
Kufewetsa gangster
Kudekhetsamo untchana
You all think about
Kupatulako Yeshua
It's you I can't live without
If you tell the homies,
I'll deny it
I won't us to chart a course
Take a vacation ku Chawe
Flex alittle and ride a horse
I ain't wanna see you cause of me
Ukukhetsa misonzi
Heeyyyeaaahhh
Yehova wandipatsa umboni
Mwaiwe ndikondwera
Wakhazikika mu mtima
Mwangamu
Wakhazikika mu mtima
Mwangamu
Ndinagwada pansi
Kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa langa duwa
Ndinagwada pansi
kupemphelera iwe
Mkazi wangwiro wakumaloto
Yehova anayankha
Siuyu wandipatsa
Langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaaa
Chokhumba
Cha Moyo wanga
Ndikuyamika ndalipeza
Langa duwa
Ooowohhhhh
Duwaaaa
Chokhumba
Cha moyo wanga
Ndikuyamika
Ndalipeza langa duwa