![Musazathe](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/04/29/efd271c8021749e2add1e27d23312967_464_464.jpg)
Musazathe Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
A mic in my hand, I relax and rewind
Ndimamenya freestlye straight from the mind (from the brain)
Ati Swanky timakukonda usazafe, apa pali bomba usaponde landmine
Ndikumveka mu ma speaker mu subwoofer, Mfana wapantunda mu gumbagumba
Bwinobwino ndikumenya. Patali tikupenya Ati Swanky usazafe bwana content creator
Umamenya bohz, umabwiza bo, mukamenya njomba fanzi imapenga
Akakhala ma chick ma team mukuchenja, chonde musazafe olo muzangopenga
I can see what they mean when they say changes, life is constantly rearranging
Love me now mama, I'm perfect now mama, zamawa siziziwika tithat kunamizana
Kuthamangitsa Gist zinthu zovaya, zomwendimapanga ndizaku Blantyre
Koma zanthumba ndizaku Lilongwe, ndakuthoka facts koma sichipongwe
Umavunga round Ase, dollar zisazathe Ase, Iweso usazathe Ase, ndati ndati chonde usazathe Ase
Chonde musazathe, chonde musazathe achimwene, chonde musazathe ndipo chonde musazafe

Ndalandila trans ID, walandila Please call me, Ati Mr. Swanky tibwelekeni Hanzi tiakhole a landlord
Apa pali swaz, apa pali Gin, uzikhalandi manyazi ukaona pin Pakakhala ma chick olo opanda ma chick uzikhala ndi nkhani usanapange speak
Ndipo usazathe umatha kucheza, nthumazi imandipeza, nkapanda kukupeza
Tsikulamacheza sitivala ma blazer, tsiku laazibambo layambila pa Keza
Ndamuthoka bar man tsitsa sound kaye, talandila phone call tavunga round kaye
Amatha kucheza awa usawatsuste, tadikila kaye my nigga uzatifuse