Sabbata Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Sabbata - Zither Harmony
...
Sunga tsiku la-ce lophatulikalo,
UM'phempetse Mwini njira yakunka m'mwambamo;
TikaM'satira Iye pa dziko lino,
Adzatipatsa madzi a moyo (madzi a moyo)...
Tikondwera kudza kwa Sabata, tsiku la cimwemwe;
Tiyamikeeee Mwini Wa yonse (Mwini wa yonse)
Tikondwera kudza kwa Sabata, tsiku la cimwemwe;
Tiyamikeeee Mwini Wa yonse
Tikondwera kudza kwa Sabata, tsiku la cimwemwe,
Tiyamikeeee Mwini Wa yonse (Mwini wa yonse)
Tikondwera kudza kwa Sabata, tsiku la cimwemwe,
Tiyamikeeee Mwini wa yonse.
(Others in background:
Ti-ti-tiyamika, ti-ti-tiyamika...)
Lead:
Mbala me ndiyamikira Mulengi Wao mitengo iwedera Mulengi Wao matsiku onseeee;
Kodi mbale iwe, siufuna kuyamikira Mulengi Wako, Mulengi Wako
Pa tsiku, pa tsiku la Sabata
(Ding-dong ding-dong)
Lead:
Ife lelo tiyamika Yesu Mpulumtsi ndi Yesu Mulengi,
Amamvatu tikapemphera Adzamveraaaaaa......
Tiiiyamika Yesu Mpurumutsi ndi Yesu Mulengi,
Amamvatu, Amamvatu tikapempheeeeraaaaa....
Amamvatu tikapempheeera...
(Others:
Tiyamikeeee, tiyamikeeee)
Lead:
Mulengi WathuYooo
Ndi Mwini Wa zinthu zonseeeii
Mulengi Wathu, Mulengi Wathu oooo
Ndi Yesu Mfumu Ya mafumu onse
Amatisamara, Amatitetedza
Tiyamike Mwine, Mfumu YathuYo
Mulengi Wathu, Mulengi Wathu ooooo
(Mwiini Wa yoonseeeeeeeee.......nseeeeee
...nseeeee)