
Yesu Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
This song is not currently available in your region.
Try the alternative versions below.
Alternative versions:
Lyrics
Yesu - Chigo Grace
...
Pachiyambi panali mawu
Mawu anali, Kwa Mulungu
Ndipo Mauwo ndiye Mulungu
Pachiyambi panali mawu
Mawu anali, Kwa Mulungu
Ndipo Mauwo ndiye Mulungu
eeh
ooh
eh eh
Mau anasandulika thupi
Nakhazikika pakati pathu
Iye ndiye kuwala ndi moyo
Zonse zinalengedwa ndi iye
Anadzikhadzikitsa mwa iye
Chilichonse chili manja mwake
Iye ndiye mwini zonse
Mphamvu ndi ulemelero
Ukulu ndi Ufumu zili zake
Oyamba otsiriza
Aliyemweyo sasintha
Iye ndiye fumu yamuyaya
Yesu ooooh Yesu ooooh
Dzina loposa ma ina onse
Mpulumutsi wa dziko lonse
Wodabwitsa mfumu yokongola
Atikonda ife kopambana
Watiyitana mu Ufumu wake
Watipatsa moyo mwa ulere
Iye ndiye mwini moyo
Moyo wamuyaya
Anagonjetsa imfa
Mfumu Yesu
Palibe omutsutsa, wopikitsana naye
Iye ndi Mulungu, mwa iye yekha
Yesu ooooh Yesu oooh oh
Dziko lonse liyenera lim'dziwe
Dziko lonse liyenera lim'landire
Dziko lonse liyenera lim'dziwe
Dziko lonse liyenera lim'landire
Ayaay ayaay ayaay ayaay
Ayaay ayaay ayaay ayaay
Iye ndiye mwini zonse
Mphamvu ndi ulemelero
Ukulu ndi Ufumu zili zake
Oyamba otsiriza
Aliyemweyo sasintha
Iye ndiye fumu yamuyaya
Yesu ooooh Yesu ooooh
Yesu yeee Yesuu oooh
Fumu ya mafumu Kalonga wa mtendere
ooh Yesu, Yesu
Fumu yokongola