
Kholo Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
In you God I find my rest
My defender and my peace
I call you abba
Ndinu kholo langa
Mulungu wosasintha mbiri
Dzulo lero mawa muli
Wamuyaya baba
Ndinu moyo wanga
Mwa imwe nkhukondwa dada
Ndinu madziko anga
Ndimwe chitemwa Dada
Abba Father
Ndinu kholo langa
My redeemer my provider
Yahweh chikonfi chanu chindikakamila
It knows no season
Mulungu wosasintha mbiri
Dzulo lero mawa muli
Wamuyaya Baba
Ndimwe fumu yane