Inu Mayi (feat. Macky 2)
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2021
Lyrics
Inu Mayi ft. Macky 2 - Goddy Zambia
...
Inu mayi Kodi mulikumva ?ah Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu Inu mayi Kodi mukumbukira Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako (Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama) VERSE (Goddy) Kodi mumadya zichani Kuvala zichani Kodi nyumba mukhalamo yo Anamanga ndani Pomwe munafa anakulandilani ndi ndani Mafunso ndi wambiri pa tisakulise nkhani Leka ndi kambe ndi yesu ambuye wanga ndinu Munawadziwa mayi anga asanakhale malemu Mwina anali muntu ochimwa pa maso panu Koma kumulanda moyo chinapweteketsa khamu Kodi munalowa m’jerusalema ? Mwina munalowako kugahena Kodi munaonana namalenga Mwinanu munango werudzika Munali ndi Ana achichepere ×2 (kudziko munasiya mayi anga? CHORUS: Inu mayi Kodi mulikumva ?ah Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu Inu mayi Kodi mukumbukira Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako (Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama) VERSE : (Macky 2) Uko kumwamba kwemulili mulungu amisunge, Apitilize chingiliza devil asanitunke Ma letter nimamilembela ninshi siyana fike Ndaba mafunso ninafunsa neo simunayanke Nikali funo ziba why munanisiya so? Tinaluvyanya chani ndaba we reap what we sow? They say celebrate life when somebody dies, but when we think of you everybody cries Dear mama! Dear mama! I can’t wait for the day yene tizakakumana. They told me limba mwamuna samalila, but chikonko mutima chaugwililila. Everything I have is all because of you, so it’s only right I sing this song for you, and if all this money can’t even bring me joy then at least let me be a Mama’s boy.
Similar Songs
More from Goddy Zambia
Listen to Goddy Zambia Inu Mayi (feat. Macky 2) MP3 song. Inu Mayi (feat. Macky 2) song from album Underrated is released in 2021. The duration of song is 00:03:52. The song is sung by Goddy Zambia.
Related Tags: Inu Mayi (feat. Macky 2), Inu Mayi (feat. Macky 2) song, Inu Mayi (feat. Macky 2) MP3 song, Inu Mayi (feat. Macky 2) MP3, download Inu Mayi (feat. Macky 2) song, Inu Mayi (feat. Macky 2) song, Underrated Inu Mayi (feat. Macky 2) song, Inu Mayi (feat. Macky 2) song by Goddy Zambia, Inu Mayi (feat. Macky 2) song download, download Inu Mayi (feat. Macky 2) MP3 song
Comments (24)
New Comments(24)
Emmanuel Ngulubeh4jbj
destiny dackson
cool [0x1f623][0x1f623][0x1f630]
mosesnzrdp
wonder why the Zambian music industry keeps underrating this guy? otherwise his fire
AGENGO SIRKAL
warm[0x1f60e]
AGENGO SIRKAL
cool[0x1f623][0x1f623][0x1f623][0x1f623]
OlawaleSupernova
Africa is going Bigger
Cͨlaͣs͛s͛iͥcͨaͣl
i love this
Flex Moolah
this i magnificent
Kenyan trending teens 254
love the beatz[0x1f621][0x1f621][0x1f621][0x1f623][0x1f623][0x1f623]
Kenyan trending teens 254
good play maker[0x1f621][0x1f621][0x1f621][0x1f623]
Stephen Mukazi
how are you doing today my friend's
This is emotional [0x1f625][0x1f607][0x1f63f][0x1f63f] I miss mum [0x1f653][0x1f653]
Stephen Mukazi
your King Soopers
Excellent❤️