
Ine Ndine Mpesa
- Genre:Gospel
- Year of Release:2025
Lyrics
Mmmmmmh ooooooh ooooooh Akuzike Thawe yeahhhhhhhhh eeh eeh
Ngati wina sakhala mwa Ine, watayika kunja monga nthambi, nafota; ndipo azisonkhanitsa nazitaya kumoto, nazitentha
Ngati mukhala mwa Ine, ndi mau anga akhala mwa inu, pemphani chilichonse chimene muchifuna ndipo chidzachitika kwa inu
Khalani mwa Ine, ndi Ine mwa inu. Monga nthambi siingathe kubala chipatso pa yokha, ngati siikhala mwampesa; motere mulibe inunso ngati simukhala mwa Ine
Ine ndine mpesa, inu ndinu nthambi zake: wakukhala mwa Ine, ndi Ine mwa iye, ameneyo abala chipatso chambiri; pakuti kopanda Ine simungathe kuchita kanthu
Mwa ichi alemekezedwa Atate wanga, kuti mubale chipatso chambiri; ndipo mudzakhala ophunzira anga. Monga momwe Atate wandikonda Ine, Inenso ndakonda inu; khalani m'chikondi changa
Khalani mwa Ine, ndi Ine mwa inu. Monga nthambi siingathe kubala chipatso pa yokha, ngati siikhala mwampesa; motere mulibe inunso ngati simukhala mwa Ine
see lyrics >>Similar Songs
More from Akuzike Thawe
Listen to Akuzike Thawe Ine Ndine Mpesa MP3 song. Ine Ndine Mpesa song from album The Year Of The Blood Of Jesus Christ is released in 2025. The duration of song is 00:03:29. The song is sung by Akuzike Thawe.
Related Tags: Ine Ndine Mpesa, Ine Ndine Mpesa song, Ine Ndine Mpesa MP3 song, Ine Ndine Mpesa MP3, download Ine Ndine Mpesa song, Ine Ndine Mpesa song, The Year Of The Blood Of Jesus Christ Ine Ndine Mpesa song, Ine Ndine Mpesa song by Akuzike Thawe, Ine Ndine Mpesa song download, download Ine Ndine Mpesa MP3 song