- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
Ambuye ndabwela, mbuye ndabwela
Kuyamikila chisomo chanu
Ambuye ndabwela, mbuye ndabwela
Kuyamikila chikondi chanu
Zikomo, zikomo, zikomo, zikomo
Zikomo, zikomo ambuye eeeeeh
Ndinali ndani popanda inu
Ndinali ndani ine eeeh popanda inu
Mwandisambitsa, mwandiyeretsa
Mwandikwezeka, mwanditukula oooh
see lyrics >>Similar Songs
More from Sarai Chimombo
Listen to Sarai Chimombo Zikomo MP3 song. Zikomo song from album Zikomo is released in 2024. The duration of song is 00:03:53. The song is sung by Sarai Chimombo.
Related Tags: Zikomo, Zikomo song, Zikomo MP3 song, Zikomo MP3, download Zikomo song, Zikomo song, Zikomo Zikomo song, Zikomo song by Sarai Chimombo, Zikomo song download, download Zikomo MP3 song