Zonse Zanga ft. Mastol
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Yeah
Ndili wamasiye munakhala kholo
Kusiya ulemelero kusankha kapolo
Mwayankha mafunso opanda ansala olo
Ntakumana ndi zokhoma muzakhalapo
Poti ndinu amene munandilipilira dipo
Mutaponde phazipo nane ndipondepo
Mundigwire mkono musandisiye ndipo
Ndikhale nanu closer ngati John, Peter ndi Paul
Mukanena "muka" ndizigalamuka
Kunka kukalalika mukangolamula dzuka
Ine pompo osalefuka
see lyrics >>Similar Songs
More from Jeremiah Chikhwaza
Listen to Jeremiah Chikhwaza Zonse Zanga ft. Mastol MP3 song. Zonse Zanga ft. Mastol song from album First Question is released in 2022. The duration of song is 00:02:58. The song is sung by Jeremiah Chikhwaza.
Related Tags: Zonse Zanga ft. Mastol, Zonse Zanga ft. Mastol song, Zonse Zanga ft. Mastol MP3 song, Zonse Zanga ft. Mastol MP3, download Zonse Zanga ft. Mastol song, Zonse Zanga ft. Mastol song, First Question Zonse Zanga ft. Mastol song, Zonse Zanga ft. Mastol song by Jeremiah Chikhwaza, Zonse Zanga ft. Mastol song download, download Zonse Zanga ft. Mastol MP3 song