
Si Business. ft. BLAZE YODELLA Lyrics
- Genre:Alternative
- Year of Release:2021
Lyrics
Musalipute banja ndi big deal
Ukwati si nthabwala za mfilimu
Funa kuyiphula msanga muli nkhwilu
Ndi ma dincam ingodekhani ah
Dziwanani naye musachite phuma
Dziwa zofowoka zake osapupuluma
Anakonda mtima Anakonda chuma
Adzakhala nawe olo mu nyengo zothuma
Musamakopeke ndi njenjete
Amakupopa ATI jentele
Akupake mwana Nde uchenjele
Sungamange banja no mtendere
Angofuna olemela ah
Bola mbumba yake udzilela
Zawo ziyele
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Si NTChito
Ife tikumanenatu adona Inu
Kuti osakwatilila kaliwonela
Zowona banja limakoma Inu
Koma zimafunika kukhonzekela
Poti banja si ganyu kuti ukatopa utha kupempha Kwa bwana holiday
Kamayamba banja muzikonzeka poti mabanja ndi onse koma quality
Ah anthu ndiye mukwatilatu
Awuze chiwamba osawabisilatu
Ena banja nailthawa
Akuti mkazi wawo akumawakawa
Amafuna wokongola
Wokongolaso amafuna wadollar
Analiyamba Dala banja
Pano banja likuwachitaso nkhaza awo
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Si NTChito
Moyo Nde mpambaaa
Osati banjaaaaa
Kumazikondaaa
Kuposa Ndalamaaaa
Moyo Nde mpambaaa
Osati banjaaaaa
Kumazikondaaa
Kuposa Ndalamaaaa ah ah ah
Moyo Nde mpambaaa
Osati banjaaaaa
Kumazikondaaa
Kuposa Ndalamaaaa
Moyo Nde mpambaaa
Osati banjaaaaa
Kumazikondaaa
Kuposa Ndalamaaaa ah ah ah
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Si NTChito
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Awo muwauze awo
Asathamangile kukwatira
Banja si Business banja si malonda
Si NTChito