
Maloto Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Ase Hyke
Yeah yeah uuuuh uuuuh
Mmmh yea yea yea yeah yeah yeah
Ooooh
Wangondigulitsa maloto
Ndasanduka chitonzo
Wandigwilitsa fuwa la moto
Ndinkadalila hane
Wangondigulitsa maloto-to
Ndasanduka chitonzo-zo
Wandigwilitsa fuwa la moto
Nkundisiya pa mphepo
Ndimadalila dalila dalila iweyo
Wangondigulitsa
Maloto loto loto malo
Maloto loto loto malo
Maloto loto loto
Maloto
Wangondigulitsa
Maloto loto loto malo
Maloto loto loto malo
Maloto loto loto malo
Ondiuza nde analipo koma kusamva kwanga
Sindinali munthu omvela malangizo
Mpake chibwana chandilanda
Why's it hard to let you go
When I know you do me dirty
Had me feeling insecure on a daily
Ask you if you still love me you said maybe
Watchu mean when you say maybe?
Mmh pano ndizo ndizo ndizo
Maso mwalenga misonzi
Ndizo Ndizo Ndizo
Wandisiya manja alinkhosi
Ndizo Ndizo Ndizo
Ndaombela mfiti manja
Chikondi chija chatha
Wangondigulitsa maloto
Ndasanduka chitonzo
Wandigwilitsa fuwa la moto
Ndinkadalila hane
Wangondigulitsa malo oooto
Ndasanduka chitonzo oooonzo
Wandigwilitsa fuwa la moto
Nkundisiya pa mphepo
Ndimadalila dalila dalila iweyo
Wangondigulitsa
Maloto