
Kalikokha Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Yeah yeah yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah yeah yeah yeaaah yeah yeah
Yeah yeah yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah yeah yeah yeaaah
TrickyBeatz
Kalikokha nkanyama
Mtima wanga wasankha iwe
Ndilole ndikukonde
Ndilole ndikukonde ndikukonde
Kalikokha nkanyama
Maso anga aona iwe
Ndizotheka ndikukonde?
Nzotheka ndikukonde?
Nyumba ikulilenji
Nsima ya munthu mmodzi koma ikusala
Chakudya sichikoma
Ndimangotaya
Maka mdima ukagwa
Mkati mwangamu umadzala nkhawa
Ndikazampeza sazandithawa ine
Mwina zachikondi zinandilaka ine
Tsano
Chikati gogogo chili pa iwe chili pa ine
Chili pa iwe chili
Ngati ngumbi londo londo
Komwe upite ndikusatile
Komwe upite ndikusatile shuwa
Gogogo chili pa iwe chili pa ine
Chili pa iwe chili pa ine
Ngati ngumbi
Komwe upite ndikusatile eh
Kalikokha nkanyama
Mtima wanga wasankha iwe
Ndilole ndikukonde
Ndilole ndikukonde ndikukonde
Kalikokha nkanyama
Maso anga aona iwe
Ndizotheka ndikukonde?
Nzotheka ndikukonde?
Zanga zonse tenga ndakupasa
Mtimau unalasa iwe dale wanga
Iwe Dale wanga
Chilichonse tenga ndakupasa
Mtima unalasa iwe Dale wanga
Iwe dale wanga
Tsano chikati gogogo chili Pa iwe chili pa ine
Chili pa iwe chili
Ngati ngumbi londo londo
Komwe upite ndikusatile
Komwe upite ndikusatile shuwa
Gogogo chili pa iwe chili pa ine
Ngati ngumbi komwe upite ndikusatile
Eh
Kalikokha nkanyama
Mtima wanga wasankha iwe ndilole ndikukonde
Ndilole ndikukonde ndikukonde
Kalikokha nkanyama
Maso anga aona iwe
Ndizotheka ndikukonde?
Nzotheka ndikukonde?
Kalikokha nkanyama
Mtima wanga wasankha iwe ndilole ndikukonde
Ndilole ndikukonde
Ndikukonde
Kalikokha nkanyama
Maso anga aona iwe
Ndizotheka ndikukonde?
Nzotheka ndikukonde?