![Olungama ft. T-sean](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/08/14/f1e8e19599ac46e2ba9c0feb2c3784b5_464_464.jpg)
Olungama ft. T-sean Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Before you
Analiponso anzako ena
Before me I know
Analiponso anzanga ena
I've been a player sindingakane
Akazi ankabwera sindingakane
Koma lero my choice is you
Ndikut lero make I live with you
And she say
I know siiwe olungama
Ulinso ndizolakwa zako
Nanenso si olungama
Ndilinso ndizolakwa zanga
Udzandikonde limodzi ndizolakwa zanga
Limodzi ndizolakwa zanga
Nzakukonde limodzi Ndizolakwa zako
Limodzi ndizolakwa zako ineyo
I love you with your flaws
Every scar and every cause
You're the one that makes me feel alright
Sindingafune wina ine awe
Masiku yanga pachalo ni yachani ngati sinili na iwe
Life yanga ilibiretu phindu ngati sinili na iwe
Girlwhen you smile
You turn my grey sky blue
You're mi number one mi can't replace you
You're di light in nah mi life
Jah jah bless you
Never ever seen deh love so deep
Woyi
I know siiwe olungama
Ulinso ndizolakwa zako
Nanenso si olungama
Ndilinso ndizolakwa zanga
Udzandikonde limodzi ndizolakwa zanga
Limodzi ndizolakwa zanga
Nzakukonde limodzi Ndizolakwa zako
Limodzi ndizolakwa zako ineyo
See I go sing am
I go sing am
I go sing an
I go sing am
I go sing am for you
See I believe and I believe
And I believe and I believe
And I'm believing in you
See I go put it on you
You go put it on me
See I'm believing in you
And you believing in me ooh
I know siiwe olungama
Ulinso ndizolakwa zako
Nanenso si olungama
Ndilinso ndizolakwa zanga
Udzandikonde limodzi ndizolakwa zanga
Limodzi ndizolakwa zanga
Nzakukonde limodzi Ndizolakwa zako
Limodzi ndizolakwa zako ineyo