Out Of My League Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
I say Beauty yofunika medal
Timaso tokoka attention
Akamayenda ngati sanachimwepo
Polenga iwe ankaona angelo
Mmaso mwanga ndamunveka velo
Koma olo Dzina langa sanalinvepo
Zoti amandidziwa sindinganenepo
Awa ndi makina machine amphepo
Uyu ndi ndimankhwala ozunguza bongo
Ona mpaka shasha wapinda mabondo
Kaya ndi nkhondo tisenza mikondo
Kaya sandinvera tikaona konko
Sangandinveeee olo ndita olo nditakuwa
Sangayimeee olo ndita olo nditakuwa
This girl is out of my league
She is out of my league
This girl is out of my league
She is out of my league
Ali champions ndili mu super league
Ndili mu disco iye super gigi
Mu bus yake sindingapezemo seat
Ndili panja sitingachite link
Call me a soldier Ndili Pa mission
Never give up Ndili ndi reason
Zikangovuta nditenga commission
Koma for now mayiwa ndi mission
Uyu ndi ndimankhwala ozunguza bongo
Ona mpaka shasha wapinda mabondo
Kaya ndi nkhondo tisenza mikondo
Kaya sandinvera tikaona konko
Sangandinveeee olo ndita olo nditakuwa
Sangayimeee olo ndita olo nditakuwa
This girl is out of my league
She is out of my league
This girl is out of my league
She is out of my league
To be honest zosiyana nzombiri
Zolekana nzambiri
Bwanji ndisiye ndingaononge mbiri
Ndazipatsa malire x2
Sangandinveeee olo ndita olo nditakuwa
Sangayimeee olo ndita olo nditakuwa
This girl is out of my league
She is out of my league
This girl is out of my league
She is out of my league