Ndiwe ft. Dizmo Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Mammawa ndimadzuka pambali ndi
Chimwemwe chimabwera nkuyang'anire
Unabadwa ndimphanvu yachikoka
Nkona sindimatha kukhale ndekha
Rich rich rich rich Mamie got melanin
Yeah you spice up my life
You're like cinnamon
Ndinkhale mose lowa mu Canaan
Ndiwe chawama
Ndiwe yemwe lesa
Anatuma mumoyo mwanga
Mtima wadekhetsa
I don't want anyone anymore
Kaliyang'ana dzuwa ndimaganizira iwe
Nkhale kuwale mwezi ndimaganizira iwe
Babe ndiwe
(Owala)
Babe ndiwe
(Aaa zenge)
Babe ndiwe eh
(Owala)
Babe ndiwe
(Aaaaa zenge)
Kaliyang'ana dzuwa ndimaganizira iwe
Nkhale kuwale mwezi ndimaganizira iwe
Babe ndiwe
(Owala)
Babe ndiwe
(Aaa zenge)
Babe ndiwe eh
(Owala)
Babe ndiwe
(Aaaaa zenge)