Pakwitana Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
Pakwitana - The Promise Zambia
...
Pakwitana mbuye wanga posiliza dzikoli pakufika siku lakuwalalo osonkana akunvela pakuona yesuo tizakondwelela nae komweko,Pakwitana mbuye wanga mbuye wanga mbuye wangaaaaa pakwitana mbuye wanga mbuye wanga mbuye wanga mbuye wanga tizakondwelela nae komweko......